Buku Lopatulika ndi baibulo lomwe lapangidwa polemekeza chikhulupiro chanu pamene mukupemphera. Mu app yi mulibemo ma advert (Ads) kapena malonda a mtundu ulionse.Â
Werengani mwa ufulu komanso mosavuta posintha maonekedwe a zilembo komanso kakulidwe ka zilembe.
Ngati muli ndi maganizo ena pa appyi, tumizani uthenga wanu ku Macintec Valley pa:
+265 88 39 57 080